logo
Lady Aika Onesimus Tsa-Leo Lulu Bucci TayGrin Beracah Gwamba Zani Challe Namadingo
Naxy B

NAXY B

Genre:Dance-Hall -|- City:Mangochi
Profile

Naxy B amakonda kumvera nyimbo zakunja za Reggae komaso za hiphop zomwe kwa iye muli mfundo zenizeni. Mu chaka cha 2020 adayamba kuphunzira kulemba nyimbo komanso kuimba. Izi zidapangitsa Naxy B kuti azikonda kumvera nyimbo zachimalawi .

Ataona kuti naye ali ndi ufulu olowa nawo mu industry, mu chaka cha 2021 analowa mu studio ndikutulutsa nyimbo yake yoyamba yomwe anapangidwa feature ndi mic combuster.

Related Songs

    advert